1 Samueli 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma Hana anali kulankhula mumtima mwake.+ Milomo yake inali kugwedera koma sanali kutulutsa mawu. Eli ataona zimenezo anaganiza kuti waledzera.+
13 Koma Hana anali kulankhula mumtima mwake.+ Milomo yake inali kugwedera koma sanali kutulutsa mawu. Eli ataona zimenezo anaganiza kuti waledzera.+