1 Samueli 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Patapita nthawi, mwamunayu Elikana anapita pamodzi ndi banja lake lonse kukapereka kwa Yehova nsembe ya pachaka+ ndi nsembe yake yalonjezo.+
21 Patapita nthawi, mwamunayu Elikana anapita pamodzi ndi banja lake lonse kukapereka kwa Yehova nsembe ya pachaka+ ndi nsembe yake yalonjezo.+