1 Samueli 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndipo ine ndikum’pereka* kwa Yehova.+ Ndam’pereka kwa Yehova masiku onse a moyo wake.” Pamenepo iye* anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi pamaso pa Yehova.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:28 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),4/2017, tsa. 5
28 Ndipo ine ndikum’pereka* kwa Yehova.+ Ndam’pereka kwa Yehova masiku onse a moyo wake.” Pamenepo iye* anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi pamaso pa Yehova.+