1 Samueli 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova ndi Wakupha ndi Wosunga moyo,+Iye ndi Wotsitsira Kumanda,+ ndiponso Woukitsa.+