1 Samueli 2:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pamenepo ndidzadziutsira wansembe wokhulupirika+ amene adzachita mogwirizana ndi zimene zili mumtima mwanga ndi zofuna zanga. Ndidzam’mangira nyumba* yokhalitsa, ndipo adzatumikira wodzozedwa wanga+ monga wansembe nthawi zonse.
35 Pamenepo ndidzadziutsira wansembe wokhulupirika+ amene adzachita mogwirizana ndi zimene zili mumtima mwanga ndi zofuna zanga. Ndidzam’mangira nyumba* yokhalitsa, ndipo adzatumikira wodzozedwa wanga+ monga wansembe nthawi zonse.