1 Samueli 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Akazungulirazungulira, anali kubwerera ku Rama,+ chifukwa kumeneko n’kumene kunali nyumba yake, ndipo anali kuweruza Isiraeli ali kumeneko. Komanso iye anamangira Yehova guwa lansembe kumeneko.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:17 Nsanja ya Olonda,3/15/2005, tsa. 22
17 Akazungulirazungulira, anali kubwerera ku Rama,+ chifukwa kumeneko n’kumene kunali nyumba yake, ndipo anali kuweruza Isiraeli ali kumeneko. Komanso iye anamangira Yehova guwa lansembe kumeneko.+