1 Samueli 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Samueli anatenga+ botolo ladothi la mafuta ndi kutsanulira mafutawo pamutu wa Sauli, n’kumupsompsona+ ndi kunena kuti: “Yehova wakudzoza iwe kukhala mtsogoleri+ wa cholowa chake.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:1 Tsanzirani, tsa. 73 Nsanja ya Olonda,1/1/2011, tsa. 27
10 Ndiyeno Samueli anatenga+ botolo ladothi la mafuta ndi kutsanulira mafutawo pamutu wa Sauli, n’kumupsompsona+ ndi kunena kuti: “Yehova wakudzoza iwe kukhala mtsogoleri+ wa cholowa chake.+