1 Samueli 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, Sauli atangotembenuka kuti asiyane ndi Samueli, Mulungu anayamba kusintha mtima wake kukhala wina,+ moti zizindikiro+ zonsezi zinayamba kuchitikadi pa tsiku limenelo.
9 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, Sauli atangotembenuka kuti asiyane ndi Samueli, Mulungu anayamba kusintha mtima wake kukhala wina,+ moti zizindikiro+ zonsezi zinayamba kuchitikadi pa tsiku limenelo.