1 Samueli 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sauli anayankha m’bale wa bambo akeyo kuti: “Anatiuza mosaphonyetsa kuti abulu aakazi anali atapezeka.” Koma iye sananene za nkhani ya ufumu imene Samueli anamuuza.+
16 Sauli anayankha m’bale wa bambo akeyo kuti: “Anatiuza mosaphonyetsa kuti abulu aakazi anali atapezeka.” Koma iye sananene za nkhani ya ufumu imene Samueli anamuuza.+