1 Samueli 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 ndi kuuza ana a Isiraeliwo kuti: “Mverani zimene Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena,+ ‘Ndine amene ndinatulutsa Isiraeli mu Iguputo,+ amenenso ndinakupulumutsani m’manja mwa Aiguputo ndi m’manja mwa maufumu onse amene anali kukuponderezani.+
18 ndi kuuza ana a Isiraeliwo kuti: “Mverani zimene Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena,+ ‘Ndine amene ndinatulutsa Isiraeli mu Iguputo,+ amenenso ndinakupulumutsani m’manja mwa Aiguputo ndi m’manja mwa maufumu onse amene anali kukuponderezani.+