1 Samueli 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako anabweretsa pafupi fuko la Benjamini malinga ndi mabanja awo, ndipo banja la Amatiri linasankhidwa.+ Pamapeto pake, Sauli mwana wa Kisi anasankhidwa.+ Choncho anayamba kum’funafuna, koma sanam’peze.
21 Kenako anabweretsa pafupi fuko la Benjamini malinga ndi mabanja awo, ndipo banja la Amatiri linasankhidwa.+ Pamapeto pake, Sauli mwana wa Kisi anasankhidwa.+ Choncho anayamba kum’funafuna, koma sanam’peze.