1 Samueli 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma anthu opanda pake+ anali kunena kuti: “Kodi ameneyu angatipulumutse bwanji?”+ Chotero anamunyoza,+ moti sanam’bweretsere mphatso iliyonse.+ Koma Sauli anangokhala chete.+
27 Koma anthu opanda pake+ anali kunena kuti: “Kodi ameneyu angatipulumutse bwanji?”+ Chotero anamunyoza,+ moti sanam’bweretsere mphatso iliyonse.+ Koma Sauli anangokhala chete.+