1 Samueli 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano zimene zinachitika n’zakuti, pamene iwo anali kulowa, ndipo Samueli ataona Eliyabu,+ nthawi yomweyo anati: “Mosakayikira wodzozedwa wake waonekera pamaso pa Yehova.” 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:6 Nsanja ya Olonda,3/1/2010, tsa. 23
6 Tsopano zimene zinachitika n’zakuti, pamene iwo anali kulowa, ndipo Samueli ataona Eliyabu,+ nthawi yomweyo anati: “Mosakayikira wodzozedwa wake waonekera pamaso pa Yehova.”