1 Samueli 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho Davide anapita kwa Sauli ndipo anali kum’tumikira.+ Sauli anam’konda kwambiri Davide, moti anakhala womunyamulira zida zake.+
21 Choncho Davide anapita kwa Sauli ndipo anali kum’tumikira.+ Sauli anam’konda kwambiri Davide, moti anakhala womunyamulira zida zake.+