1 Samueli 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ine ndipita nawo kutchire kumene ukabisaleko ndipo ndikaima pafupi ndi bambo anga. Bambo anga ndilankhula nawo za iwe, ndipo ndionetsetsa zimene zichitike. Zilizonse zimene ndaonazo ndidzakuuza, sindilephera.”+
3 Ine ndipita nawo kutchire kumene ukabisaleko ndipo ndikaima pafupi ndi bambo anga. Bambo anga ndilankhula nawo za iwe, ndipo ndionetsetsa zimene zichitike. Zilizonse zimene ndaonazo ndidzakuuza, sindilephera.”+