1 Samueli 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno mzimu woipa wa Yehova+ unayamba kugwira ntchito pa Sauli ali m’nyumba mwake, atatenga mkondo m’manja mwake. Pa nthawiyi, Davide anali kumuimbira nyimbo.
9 Ndiyeno mzimu woipa wa Yehova+ unayamba kugwira ntchito pa Sauli ali m’nyumba mwake, atatenga mkondo m’manja mwake. Pa nthawiyi, Davide anali kumuimbira nyimbo.