-
1 Samueli 19:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Sauli atamuuza zimenezi, nthawi yomweyo anatumiza amithenga ena, ndipo nawonso anayamba kuchita zinthu ngati aneneri. Zitatero, Sauli anatumiza amithenga enanso, gulu lachitatu, koma amenewanso anayamba kuchita zinthu ngati aneneri.
-