1 Samueli 19:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamenepo anapitiriza ulendo wake wopita ku Nayoti, ku Rama, ndipo mzimu+ wa Mulungu unafika ngakhalenso pa iye. Zitatero, iye anapitiriza kuyenda ndi kuchita zinthu ngati mneneri mpaka kukafika ku Nayoti, ku Rama.
23 Pamenepo anapitiriza ulendo wake wopita ku Nayoti, ku Rama, ndipo mzimu+ wa Mulungu unafika ngakhalenso pa iye. Zitatero, iye anapitiriza kuyenda ndi kuchita zinthu ngati mneneri mpaka kukafika ku Nayoti, ku Rama.