1 Samueli 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo Davide anauza Ahimeleki wansembe kuti: “Mfumu yandituma nkhani inayake,+ ndipo yandiuza kuti, ‘Usauze munthu aliyense nkhani imene ndikukutuma ndi zimene ndakulamula.’ Choncho ndapangana ndi anyamata kuti ndikumane nawo pamalo enaake.
2 Pamenepo Davide anauza Ahimeleki wansembe kuti: “Mfumu yandituma nkhani inayake,+ ndipo yandiuza kuti, ‘Usauze munthu aliyense nkhani imene ndikukutuma ndi zimene ndakulamula.’ Choncho ndapangana ndi anyamata kuti ndikumane nawo pamalo enaake.