1 Samueli 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma wansembeyo anayankha Davide kuti: “Ndilibe mkate wamba, koma pali mkate wopatulika.+ Nditha kukupatsa umenewu ngati anyamatawo ayesetsa kudzisunga osagona ndi akazi.”+
4 Koma wansembeyo anayankha Davide kuti: “Ndilibe mkate wamba, koma pali mkate wopatulika.+ Nditha kukupatsa umenewu ngati anyamatawo ayesetsa kudzisunga osagona ndi akazi.”+