-
1 Samueli 21:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Wansembeyo poyankha anati: “Lupanga la Goliyati+ Mfilisiti amene unamukantha m’chigwa cha Ela+ lilipo. Lakulungidwa ndi nsalu ndipo lili kuseli kwa efodi.+ Ngati ungakonde kutenga limeneli, litenge, chifukwa palibenso lupanga lina.” Pamenepo Davide anati: “Palibe lina lingafanane nalo, ndipatseni limenelo.”
-