-
1 Samueli 21:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Pamapeto pake Akisi anauza atumiki ake kuti: “Mukuona kuti munthuyu ndi wamisala. N’chifukwa chiyani mwabwera naye kwa ine?
-