1 Samueli 26:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Davide anapitiriza kunena kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ Yehova iye mwini adzamukantha,+ kapena tsiku lidzafika+ ndipo adzamwalira mmene amachitira wina aliyense, kapenanso adzapita kunkhondo+ ndipo adzaphedwa kumeneko.+
10 Davide anapitiriza kunena kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ Yehova iye mwini adzamukantha,+ kapena tsiku lidzafika+ ndipo adzamwalira mmene amachitira wina aliyense, kapenanso adzapita kunkhondo+ ndipo adzaphedwa kumeneko.+