2 Samueli 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kuchokera tsiku limene ndinatulutsa ana a Isiraeli mu Iguputo kufikira lero,+ sindinakhalepo m’nyumba koma nthawi zonse ndinali kuyenda+ m’chihema chopatulika.+
6 Kuchokera tsiku limene ndinatulutsa ana a Isiraeli mu Iguputo kufikira lero,+ sindinakhalepo m’nyumba koma nthawi zonse ndinali kuyenda+ m’chihema chopatulika.+