2 Samueli 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ine ndidzakhala ndi iwe kulikonse kumene udzapite,+ ndipo ndidzawononga ndi kuchotsa adani ako onse pamaso pako.+ Ndidzakupangira dzina lotchuka,+ lofanana ndi dzina la anthu otchuka amene ali m’dziko.
9 Ine ndidzakhala ndi iwe kulikonse kumene udzapite,+ ndipo ndidzawononga ndi kuchotsa adani ako onse pamaso pako.+ Ndidzakupangira dzina lotchuka,+ lofanana ndi dzina la anthu otchuka amene ali m’dziko.