2 Samueli 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo anthu anga Aisiraeli ndidzawasankhira malo+ ndi kuwakhazika+ pamalowo. Iwo adzakhaladi kumeneko ndipo sadzasokonezedwanso. Anthu osalungama sadzawasautsanso ngati mmene anachitira poyamba,+
10 Ndipo anthu anga Aisiraeli ndidzawasankhira malo+ ndi kuwakhazika+ pamalowo. Iwo adzakhaladi kumeneko ndipo sadzasokonezedwanso. Anthu osalungama sadzawasautsanso ngati mmene anachitira poyamba,+