2 Samueli 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo kukoma mtima kwanga kosatha sikudzachoka pa iye monga mmene ndinakuchotsera pa Sauli,+ amene ndinam’chotsa pamaso pako.
15 Ndipo kukoma mtima kwanga kosatha sikudzachoka pa iye monga mmene ndinakuchotsera pa Sauli,+ amene ndinam’chotsa pamaso pako.