2 Samueli 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Tsopano inu Yehova Mulungu, chitani mpaka kalekale mawu amene mwalankhula okhudza mtumiki wanu ndi nyumba yake. Chitani mmene mwanenera.+
25 “Tsopano inu Yehova Mulungu, chitani mpaka kalekale mawu amene mwalankhula okhudza mtumiki wanu ndi nyumba yake. Chitani mmene mwanenera.+