2 Samueli 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Dzina lanu likwezeke mpaka kalekale.+ Anthu anene kuti, ‘Yehova wa makamu ndi Mulungu wa Isiraeli,’+ ndipo nyumba ya mtumiki wanu Davide ikhazikike pamaso panu.+
26 Dzina lanu likwezeke mpaka kalekale.+ Anthu anene kuti, ‘Yehova wa makamu ndi Mulungu wa Isiraeli,’+ ndipo nyumba ya mtumiki wanu Davide ikhazikike pamaso panu.+