2 Samueli 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zimenezi zinam’vutitsa maganizo kwambiri Aminoni, moti anadwala+ chifukwa cha mlongo wake Tamara. Popeza Tamara anali namwali, zinali zovuta kwambiri+ kwa Aminoni kuti achite naye kalikonse.+
2 Zimenezi zinam’vutitsa maganizo kwambiri Aminoni, moti anadwala+ chifukwa cha mlongo wake Tamara. Popeza Tamara anali namwali, zinali zovuta kwambiri+ kwa Aminoni kuti achite naye kalikonse.+