2 Samueli 13:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamenepo atumiki a Abisalomu anachitira Aminoni monga mmene Abisalomuyo anawalamulira.+ Zitatero, ana onse a mfumu ananyamuka ndipo aliyense anakwera nyulu* yake ndi kuthawa.
29 Pamenepo atumiki a Abisalomu anachitira Aminoni monga mmene Abisalomuyo anawalamulira.+ Zitatero, ana onse a mfumu ananyamuka ndipo aliyense anakwera nyulu* yake ndi kuthawa.