2 Samueli 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno mfumu inauza mkaziyo kuti: “Pita kunyumba kwako ndipo ine ndisamalira nkhani imeneyi.”+