2 Samueli 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno Abisalomu anali kupitiriza kunena kuti: “Haa! Zikanakhalatu bwino ndikanaikidwa kukhala woweruza m’dziko lino+ kuti munthu aliyense wokhala ndi mlandu kapena wofuna chiweruzo azibwera kwa ine, ndipo ndikanamuchitira chilungamo.”+
4 Ndiyeno Abisalomu anali kupitiriza kunena kuti: “Haa! Zikanakhalatu bwino ndikanaikidwa kukhala woweruza m’dziko lino+ kuti munthu aliyense wokhala ndi mlandu kapena wofuna chiweruzo azibwera kwa ine, ndipo ndikanamuchitira chilungamo.”+