2 Samueli 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno zimene zinali kuchitikanso n’zakuti, munthu akafika pafupi kuti amuweramire, Abisalomu anali kutambasula dzanja lake ndi kumugwira+ kenako n’kumupsompsona.
5 Ndiyeno zimene zinali kuchitikanso n’zakuti, munthu akafika pafupi kuti amuweramire, Abisalomu anali kutambasula dzanja lake ndi kumugwira+ kenako n’kumupsompsona.