2 Samueli 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti ine mtumiki wanu ndinalonjeza lonjezo lalikulu+ pamene ndinali kukhala ku Gesuri,+ ku Siriya, ndipo ndinati, ‘Yehova akandilola kubwerera ku Yerusalemu, ndiyenera kupereka nsembe kwa Yehova.’”+
8 Pakuti ine mtumiki wanu ndinalonjeza lonjezo lalikulu+ pamene ndinali kukhala ku Gesuri,+ ku Siriya, ndipo ndinati, ‘Yehova akandilola kubwerera ku Yerusalemu, ndiyenera kupereka nsembe kwa Yehova.’”+