2 Samueli 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho mfumu inanyamuka ndi kutuluka ndipo anthu onse a m’nyumba yake anaitsatira.+ Koma mfumuyo inasiya akazi 10, amene anali adzakazi ake,+ kuti asamalire nyumba.
16 Choncho mfumu inanyamuka ndi kutuluka ndipo anthu onse a m’nyumba yake anaitsatira.+ Koma mfumuyo inasiya akazi 10, amene anali adzakazi ake,+ kuti asamalire nyumba.