2 Samueli 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kumeneko atumiki onse a mfumu, Akereti onse ndi Apeleti+ onse, anali kudutsa pamaso pake. Komanso Agiti+ onse, amuna 600 amene anamutsatira* kuchokera ku Gati+ anali kudutsa pamaso pake.
18 Kumeneko atumiki onse a mfumu, Akereti onse ndi Apeleti+ onse, anali kudutsa pamaso pake. Komanso Agiti+ onse, amuna 600 amene anamutsatira* kuchokera ku Gati+ anali kudutsa pamaso pake.