2 Samueli 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako mfumu inauza Itai+ Mgiti kuti: “Kodi iweyo ukupita nafe chifukwa chiyani? Bwerera+ ukakhale ndi mfumu, pakuti ndiwe mlendo komanso ndiwe wothawa kwanu. 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:19 Nsanja ya Olonda,5/15/2009, tsa. 27
19 Kenako mfumu inauza Itai+ Mgiti kuti: “Kodi iweyo ukupita nafe chifukwa chiyani? Bwerera+ ukakhale ndi mfumu, pakuti ndiwe mlendo komanso ndiwe wothawa kwanu.