2 Samueli 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pamenepo Davide anauza Itai+ kuti: “Dutsa, upite.” Choncho Itai Mgiti anadutsa pamaso pake komanso amuna onse amene anali kuyenda naye ndi ana onse amene anali naye.
22 Pamenepo Davide anauza Itai+ kuti: “Dutsa, upite.” Choncho Itai Mgiti anadutsa pamaso pake komanso amuna onse amene anali kuyenda naye ndi ana onse amene anali naye.