2 Samueli 15:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma ukabwerera kumzinda ndi kukauza Abisalomu kuti, ‘Inu Mfumu ine ndine mtumiki wanu. Kale ndinali mtumiki wa bambo anu, koma tsopano ndine mtumiki wanu,’+ pamenepo ukanditsutsire+ malangizo a Ahitofeli.
34 Koma ukabwerera kumzinda ndi kukauza Abisalomu kuti, ‘Inu Mfumu ine ndine mtumiki wanu. Kale ndinali mtumiki wa bambo anu, koma tsopano ndine mtumiki wanu,’+ pamenepo ukanditsutsire+ malangizo a Ahitofeli.