1 Mafumu 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Aliyense anali kubweretsa mphatso+ chaka chilichonse+ monga zinthu zasiliva,+ zinthu zagolide, zovala, zida zankhondo,+ mafuta a basamu, mahatchi, ndi nyulu.+
25 Aliyense anali kubweretsa mphatso+ chaka chilichonse+ monga zinthu zasiliva,+ zinthu zagolide, zovala, zida zankhondo,+ mafuta a basamu, mahatchi, ndi nyulu.+