1 Mafumu 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mayiyo ataona zimenezi, anauza Eliya kuti: “Ndili nanu chiyani+ inu munthu wa Mulungu woona? Mwabwera kwa ine kudzandikumbutsa cholakwa changa+ ndi kudzapha mwana wanga.” 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:18 Nsanja ya Olonda,2/15/2014, tsa. 15
18 Mayiyo ataona zimenezi, anauza Eliya kuti: “Ndili nanu chiyani+ inu munthu wa Mulungu woona? Mwabwera kwa ine kudzandikumbutsa cholakwa changa+ ndi kudzapha mwana wanga.”