1 Mafumu 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsopano Eliya anatenga mwanayo n’kutsika naye kuchokera kuchipinda chapadenga chija, n’kumupereka kwa mayi ake. Ndiyeno anati: “Taona, mwana wako ali moyo.”+
23 Tsopano Eliya anatenga mwanayo n’kutsika naye kuchokera kuchipinda chapadenga chija, n’kumupereka kwa mayi ake. Ndiyeno anati: “Taona, mwana wako ali moyo.”+