1 Mafumu 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Patapita masiku ambiri,+ mawu a Yehova anafikira Eliya m’chaka chachitatu, kuti: “Pita ukaonekere kwa Ahabu, chifukwa ndikufuna kubweretsa mvula padziko lapansi.”+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:1 Nsanja ya Olonda,4/1/2008, tsa. 194/1/1992, tsa. 17
18 Patapita masiku ambiri,+ mawu a Yehova anafikira Eliya m’chaka chachitatu, kuti: “Pita ukaonekere kwa Ahabu, chifukwa ndikufuna kubweretsa mvula padziko lapansi.”+