1 Mafumu 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chotero Eliya anapita kukaonekera kwa Ahabu. Pa nthawiyi n’kuti njala itafika poipa kwambiri+ ku Samariya.
2 Chotero Eliya anapita kukaonekera kwa Ahabu. Pa nthawiyi n’kuti njala itafika poipa kwambiri+ ku Samariya.