1 Mafumu 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma Obadiya anati: “Kodi ndachita tchimo lanji+ kuti mupereke mtumiki wanune m’manja mwa Ahabu kuti andiphe?
9 Koma Obadiya anati: “Kodi ndachita tchimo lanji+ kuti mupereke mtumiki wanune m’manja mwa Ahabu kuti andiphe?