1 Mafumu 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi mbuye wanga simunamve zimene ndinachita pamene Yezebeli anapha aneneri a Yehova? Ndinabisa aneneri 100 a Yehova m’phanga.+ Ndinawagawa m’magulu awiri a aneneri 50 gulu lililonse, ndipo ndinali kuwapatsa mkate ndi madzi.+
13 Kodi mbuye wanga simunamve zimene ndinachita pamene Yezebeli anapha aneneri a Yehova? Ndinabisa aneneri 100 a Yehova m’phanga.+ Ndinawagawa m’magulu awiri a aneneri 50 gulu lililonse, ndipo ndinali kuwapatsa mkate ndi madzi.+