1 Mafumu 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho Ahabu anatumiza uthenga kwa ana onse a Isiraeli, n’kusonkhanitsanso aneneri+ paphiri la Karimeli.
20 Choncho Ahabu anatumiza uthenga kwa ana onse a Isiraeli, n’kusonkhanitsanso aneneri+ paphiri la Karimeli.