1 Mafumu 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako muitane dzina la mulungu wanu.+ Inenso ndiitana dzina la Yehova, ndipo Mulungu amene ayankhe potumiza moto+ ndiye Mulungu woona.”+ Anthu onsewo atamva zimenezi anayankha kuti: “Zili bwino.”
24 Kenako muitane dzina la mulungu wanu.+ Inenso ndiitana dzina la Yehova, ndipo Mulungu amene ayankhe potumiza moto+ ndiye Mulungu woona.”+ Anthu onsewo atamva zimenezi anayankha kuti: “Zili bwino.”