1 Mafumu 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iwo anayamba kuitana mokuwa kwambiri n’kumadzicheka+ ndi mipeni ndi mikondo ing’onoing’ono malinga ndi mwambo wawo, mpaka magazi anayamba kutuluka ndi kuyenderera pamatupi awo. 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:28 Nsanja ya Olonda,1/1/1998, tsa. 30
28 Iwo anayamba kuitana mokuwa kwambiri n’kumadzicheka+ ndi mipeni ndi mikondo ing’onoing’ono malinga ndi mwambo wawo, mpaka magazi anayamba kutuluka ndi kuyenderera pamatupi awo.